Текстов песен в базе: 1 278 222
Udani

Udani

NdineZulu

Текст песни

Kudabwa
Nthawi zina ndima dabwa
Wanga anthu momwe ama khala
Kubaba mtima wanga uma baba
Ubaba anthu zomwe ama panga
Kudana anthu awa ama dana
Sibanja ine mango khala
Mwina ndi nyanga zomwe wina ana panga
Kapena sinyanga nakuba kapena chabe nikaduka
Kamene kalengesa banthu bamozi kupeza vifukwa
Cifukwa mayeso fufuza koma sina peze cifukwa eh
Kunjako nko kudha macita mantha ndi khalidwe yawa
Udani waconco wacoka kuti ma lankhulana
Pempelo yanga niyoti izozo ma lalilane
Nanga cikondi munali naco cinapita kuti
Funso
Kudabwa
Nthawi zina ndima dabwa
Wanga anthu momwe ama khala
Kubaba mtima wanga uma baba
Ubaba anthu zomwe ama panga
Kudana anthu awa ama dana
Sibanja ine mango khala
Kumakhalila midesu
Ena akulila Yesu
Mundisamalile ana banja isa pwasuke tikhale ifeso
Ogwilizana despite what we facing I hope we don’t break us ineo
Pemphelo yanga ndiyoti udani ulipo kuntima uthepo
Koma zukhala nga e sizotheka anthuwa afuna afepo
Udani waconco ku opya Ambuye kumwamba muyanganilepo
Kuma kangana pa zopanda phindu poka poka ena afepo
Anthu wa ndani aloza umbuli wa conci ine sina onepo
Kudabwa
Nthawi zina ndima dabwa
Wanga anthu momwe ama khala
Kubaba mtima wanga uma baba
Ubaba anthu zomwe ama panga
Kudana anthu awa ama dana
Sibanja ine mango khala
Поделиться ссылкой:
Короткая ссылка: https://tekstpesni.ru/s/bkY
© 2017–2025 Тексты песен
Все тексты песен на сайте размещены пользователями, редакцией или собраны из открытых источников.
При копировании материалов ссылка на сайт обязательна.
Связаться
Уважаемые обладатели прав на музыку! На сайте не выкладывается музыка, ее нельзя скачать, послушать и тому подобное.